Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Pakuti gawo la Yehova ndilo anthu ake.+

      Yakobo ndiye gawo la cholowa chake.+

  • Amosi 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 ‘Pa mabanja onse apadziko lapansi+ ine ndimadziwa inu nokha.+ Choncho ndidzakulangani chifukwa cha zolakwa zanu zonse.+

  • Malaki 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Iwo adzakhala anthu anga,+ pa tsiku limene ndidzawasandutse chuma chapadera,”+ watero Yehova wa makamu. “Ndidzawachitira chifundo monga mmene munthu amachitira chifundo mwana wake amene amamutumikira.+

  • 1 Petulo 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma inu ndinu “fuko losankhidwa mwapadera, ansembe achifumu, mtundu woyera,+ anthu odzakhala chuma chapadera,+ kuti mulengeze makhalidwe abwino kwambiri”+ a amene anakuitanani kuchoka mu mdima kulowa m’kuwala kwake kodabwitsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena