Ezekieli 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Ku Mandako, atsogoleri a anthu amphamvu adzalankhula ndi iyeyo komanso amene anali kumuthandiza.+ Onsewo adzatsikira kumanda.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga ndipo adzaikidwa m’manda mofanana ndi anthu osadulidwa.
21 “‘Ku Mandako, atsogoleri a anthu amphamvu adzalankhula ndi iyeyo komanso amene anali kumuthandiza.+ Onsewo adzatsikira kumanda.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga ndipo adzaikidwa m’manda mofanana ndi anthu osadulidwa.