Yobu 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti ndinkapulumutsa wosautsika wopempha thandizo,+Ndiponso mwana wamasiye* ndi aliyense amene analibe womuthandiza.+ Salimo 72:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aweruzire anthu milandu mwachilungamo,+Ndipo aweruze milandu ya osautsika ndi ziweruzo zolungama.+ Yesaya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+
12 Pakuti ndinkapulumutsa wosautsika wopempha thandizo,+Ndiponso mwana wamasiye* ndi aliyense amene analibe womuthandiza.+
17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+