Ekisodo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo.”+ Nthawi yomweyo Mose anatenga mawu a anthuwo ndi kubwerera nawo kwa Yehova.+ 1 Mbiri 9:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Amenewa ndiwo anali oimba,+ atsogoleri a makolo a Alevi m’zipinda zodyera.+ Iwo sanali kupatsidwa ntchito zina+ chifukwa usana ndi usiku anali ndi udindo wogwira ntchito yawo.+ Nehemiya 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi izi si zimene makolo anu anachita,+ mwakuti Mulungu wathu anadzetsa tsoka lonseli+ pa ife komanso pamzinda uwu? Koma inu mukuwonjezera kuyaka kwa mkwiyo wake pa Isiraeli mwa kuipitsa sabata.”+
8 Kenako anthu onse anayankhira pamodzi kuti: “Zonse zimene Yehova wanena tidzachita zomwezo.”+ Nthawi yomweyo Mose anatenga mawu a anthuwo ndi kubwerera nawo kwa Yehova.+
33 Amenewa ndiwo anali oimba,+ atsogoleri a makolo a Alevi m’zipinda zodyera.+ Iwo sanali kupatsidwa ntchito zina+ chifukwa usana ndi usiku anali ndi udindo wogwira ntchito yawo.+
18 Kodi izi si zimene makolo anu anachita,+ mwakuti Mulungu wathu anadzetsa tsoka lonseli+ pa ife komanso pamzinda uwu? Koma inu mukuwonjezera kuyaka kwa mkwiyo wake pa Isiraeli mwa kuipitsa sabata.”+