Yeremiya 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Anthu awa, aneneri, kapena ansembe akakufunsa kuti, ‘Kodi uthenga* wa Yehova ukuti chiyani?’+ uwayankhe kuti, ‘“Anthu inu ndinu katundu wolemetsa!+ Ndipo ndidzakusiyani,”+ watero Yehova.’ Maliro 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 N’chifukwa chiyani mwatiiwala kwamuyaya+ ndi kutisiya kwa masiku ambiri?+
33 “Anthu awa, aneneri, kapena ansembe akakufunsa kuti, ‘Kodi uthenga* wa Yehova ukuti chiyani?’+ uwayankhe kuti, ‘“Anthu inu ndinu katundu wolemetsa!+ Ndipo ndidzakusiyani,”+ watero Yehova.’