11 kuti a nyumba ya Isiraeli asadzasiyenso kunditsatira n’kumangoyenda uku ndi uku,+ ndiponso kuti asadzadziipitsenso ndi zochimwa zawo zonse. Chotero iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+