Yeremiya 44:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Simunadzichepetse kufikira lero+ ndipo simunachite mantha,+ kapena kutsatira malamulo+ ndi malangizo amene ndinapatsa inu ndi makolo anu.’+
10 Simunadzichepetse kufikira lero+ ndipo simunachite mantha,+ kapena kutsatira malamulo+ ndi malangizo amene ndinapatsa inu ndi makolo anu.’+