1 Mafumu 1:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Nthawi yomweyo Benaya mwana wa Yehoyada anayankha mfumu kuti: “Zikhale momwemo!*+ Yehova, Mulungu wa mbuyanga mfumu, atsimikizire zimenezi.+ Salimo 41:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+Kuyambira kalekale mpaka kalekale.+Ame! Ame!*+ Yeremiya 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kuti ndikwaniritse lumbiro limene ndinalumbirira makolo anu+ kuti ndidzawapatsa dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ monga mmene zilili lero.’”’” Pamenepo ine ndinayankha kuti: “Zikhale momwemo,* inu Yehova.” 2 Akorinto 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiponso malonjezo a Mulungu, kaya akhale ochuluka chotani,+ akhala Inde kudzera mwa iye.+ Choteronso kudzera mwa iye, “Ame”+ amanenedwa kwa Mulungu kuti Mulungu alandire ulemerero kudzera mwa ife.
36 Nthawi yomweyo Benaya mwana wa Yehoyada anayankha mfumu kuti: “Zikhale momwemo!*+ Yehova, Mulungu wa mbuyanga mfumu, atsimikizire zimenezi.+
5 kuti ndikwaniritse lumbiro limene ndinalumbirira makolo anu+ kuti ndidzawapatsa dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ monga mmene zilili lero.’”’” Pamenepo ine ndinayankha kuti: “Zikhale momwemo,* inu Yehova.”
20 Ndiponso malonjezo a Mulungu, kaya akhale ochuluka chotani,+ akhala Inde kudzera mwa iye.+ Choteronso kudzera mwa iye, “Ame”+ amanenedwa kwa Mulungu kuti Mulungu alandire ulemerero kudzera mwa ife.