Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 17:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Choncho dalitsani nyumba ya mtumiki wanu kuti ikhazikike pamaso panu mpaka kalekale.+ Pakuti inu Yehova mwadalitsa nyumba ya mtumiki wanu, ndipo yadalitsika mpaka kalekale.”+

  • Yeremiya 11:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 kuti ndikwaniritse lumbiro limene ndinalumbirira makolo anu+ kuti ndidzawapatsa dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ monga mmene zilili lero.’”’”

      Pamenepo ine ndinayankha kuti: “Zikhale momwemo,* inu Yehova.”

  • Yeremiya 28:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 inde, Yeremiya anayankha kuti: “Zikhale momwemo!*+ Yehova achitedi zimenezo! Yehova akwaniritse zonse zimene walosera m’mawu ako. Achite zimenezo mwa kubwezeretsa pamalo ano ziwiya za m’nyumba ya Yehova ndi anthu onse amene anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo!+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena