Yeremiya 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamenepo Yeremiya anafunsa Mfumu Zedekiya kuti: “Kodi ineyo ndakulakwirani chiyani pamodzi ndi atumiki anu ndiponso anthu onse,+ kuti munditsekere m’ndende? Aheberi 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ena analandira mayesero awo mwa kutonzedwa ndi kukwapulidwa, komanso kuposa pamenepo, mwa maunyolo+ ndi ndende.+
18 Pamenepo Yeremiya anafunsa Mfumu Zedekiya kuti: “Kodi ineyo ndakulakwirani chiyani pamodzi ndi atumiki anu ndiponso anthu onse,+ kuti munditsekere m’ndende?
36 Ena analandira mayesero awo mwa kutonzedwa ndi kukwapulidwa, komanso kuposa pamenepo, mwa maunyolo+ ndi ndende.+