Yeremiya 35:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho ife timamvera mawu a Yehonadabu mwana wa Rekabu kholo lathu, pa chilichonse chimene anatilamula.+ Timachita zimenezi mwa kupewa kumwa vinyo masiku onse a moyo wathu, ifeyo, akazi athu, ana athu aamuna ndi ana athu aakazi.+
8 Choncho ife timamvera mawu a Yehonadabu mwana wa Rekabu kholo lathu, pa chilichonse chimene anatilamula.+ Timachita zimenezi mwa kupewa kumwa vinyo masiku onse a moyo wathu, ifeyo, akazi athu, ana athu aamuna ndi ana athu aakazi.+