Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+

  • Miyambo 29:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+

  • Yeremiya 19:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndikubweretsera mzinda uwu ndi mizinda yake yonse yozungulira masoka onse amene ndinanena, chifukwa anthu ake aumitsa khosi lawo kuti asamvere mawu anga.’”+

  • Yeremiya 35:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Choncho Yehova, Mulungu wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Tsopano Yuda ndi anthu onse okhala mu Yerusalemu ndiwagwetsera masoka onse amene ndanena.+ Ndichita zimenezi chifukwa ndalankhula nawo koma sanandimvere ndipo ndinali kuwaitana koma sanandiyankhe.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena