Yeremiya 38:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano Ebedi-meleki Mwitiyopiya,*+ amene anali nduna m’nyumba ya mfumu, ndipo pa nthawiyo anali m’nyumbamo, anamva kuti Yeremiya amuponya m’chitsime. Apa n’kuti mfumu itakhala pansi ku Chipata cha Benjamini.+
7 Tsopano Ebedi-meleki Mwitiyopiya,*+ amene anali nduna m’nyumba ya mfumu, ndipo pa nthawiyo anali m’nyumbamo, anamva kuti Yeremiya amuponya m’chitsime. Apa n’kuti mfumu itakhala pansi ku Chipata cha Benjamini.+