Yeremiya 43:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+ Yeremiya 46:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Nenani zimenezi mu Iguputo amuna inu. Lengezani zimenezi ku Migidoli,+ ku Nofi+ ndi ku Tahapanesi.+ Nenani kuti, ‘Imani chilili. Konzekani.+ Pakuti lupanga lidzawononga chilichonse chokuzungulirani.+
7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+
14 “Nenani zimenezi mu Iguputo amuna inu. Lengezani zimenezi ku Migidoli,+ ku Nofi+ ndi ku Tahapanesi.+ Nenani kuti, ‘Imani chilili. Konzekani.+ Pakuti lupanga lidzawononga chilichonse chokuzungulirani.+