Ekisodo 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwapemerera mpweya wanu,+ ndipo nyanja yawamiza.+Amira ngati mtovu m’madzi akuya.+ Oweruza 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mtsinje wa Kisoni unawakokolola,+Mtsinje wakalekale, mtsinje wa Kisoni.+Moyo wangawe, unapondereza adani amphamvu.+ Salimo 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zingwe za imfa zinandikulunga,+Chikhamu cha anthu opanda pake chinali kundiopseza.+
21 Mtsinje wa Kisoni unawakokolola,+Mtsinje wakalekale, mtsinje wa Kisoni.+Moyo wangawe, unapondereza adani amphamvu.+