Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 36:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Zimenezi zinachitika pokwaniritsa mawu a Yehova amene ananena kudzera mwa Yeremiya,+ mpaka pamene dzikolo linalipira masabata ake.+ Masiku onse amene dzikolo linali bwinja linali kusunga sabata mpaka linakwaniritsa zaka 70.+

  • Yesaya 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo ndinafunsa kuti: “Mpaka liti, Yehova?”+ Iye anayankha kuti: “Mpaka mizinda yawo itawonongedwa n’kukhala bwinja, yopanda wokhalamo. Mpaka nyumba zawo zitakhala zopanda anthu okhalamo, ndiponso mpaka nthaka itawonongekeratu.+

  • Yeremiya 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Cholowa changacho achisandutsa bwinja+ moti chafota ndipo chawonongeka.+ Dziko lonse lakhala bwinja ndipo palibe aliyense amene zikumukhudza.+

  • Ezekieli 33:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Dzikolo ndidzalisandutsa bwinja+ ndiponso malo owonongeka. Ndidzathetsa mphamvu zimene dzikolo limanyadira.+ Mapiri a mu Isiraeli adzawonongedwa+ ndipo sipadzapezeka wodutsamo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena