Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Atasamuka kumeneko anakamanga msasa m’dera la chigwa cha Arinoni,+ m’chipululu chochokera kumalire a dziko la Aamori. Chigwa cha Arinoni chinali malire pakati pa dziko la Mowabu ndi la Aamori.

  • Yoswa 13:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Cholowa chawo chinayambira kumzinda wa Aroweli+ umene uli m’mphepete mwa chigwa cha Arinoni,+ ndiponso mzinda umene uli pakati pa chigwacho, kuphatikizapo malo onse okwererapo a Medeba+ mpaka kukafika ku Diboni.+

  • Oweruza 11:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pamene anali kudutsa m’chipululu, anayenda molambalala dziko la Edomu+ ndi dziko la Mowabu, moti anadutsa chakum’mawa kwa dziko la Mowabu+ ndi kukamanga misasa m’chigawo cha Arinoni. Iwo sanadutse malire a Mowabu,+ chifukwa Arinoni ndiye anali malire a Mowabu.+

  • Yesaya 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotero Mowabu adzalira mofuula chifukwa cha tsoka lake. Aliyense wokhala m’Mowabu ndithu adzalira mofuula.+ Omenyedwawo adzalirira mphesa zouma zoumba pamodzi za ku Kiri-hareseti,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena