Yesaya 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 amene anali kumenya mwaukali anthu a mitundu yosiyanasiyana powakwapula mosalekeza,+ ndiponso amene anali kugonjetsa mitundu ya anthu mokwiya, ndi chizunzo chopanda malire.+ Yesaya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinanyoza cholowa changa+ ndipo ndinawapereka m’manja mwako.+ Iwe sunawachitire chifundo.+ Munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+ Yeremiya 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho, onse okuwononga adzawonongedwa,+ ndipo adani ako onse adzatengedwa kupita ku ukapolo.+ Amene akulanda katundu wako nawonso adzalandidwa katundu wawo. Onse ofunkha zinthu zako nawonso zinthu zawo zidzafunkhidwa.”+
6 amene anali kumenya mwaukali anthu a mitundu yosiyanasiyana powakwapula mosalekeza,+ ndiponso amene anali kugonjetsa mitundu ya anthu mokwiya, ndi chizunzo chopanda malire.+
6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinanyoza cholowa changa+ ndipo ndinawapereka m’manja mwako.+ Iwe sunawachitire chifundo.+ Munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+
16 Choncho, onse okuwononga adzawonongedwa,+ ndipo adani ako onse adzatengedwa kupita ku ukapolo.+ Amene akulanda katundu wako nawonso adzalandidwa katundu wawo. Onse ofunkha zinthu zako nawonso zinthu zawo zidzafunkhidwa.”+