Yesaya 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’Babulo simudzakhalanso anthu,+ ndipo iye sadzakhalaponso ku mibadwomibadwo.+ Kumeneko Mluya sadzakhomako hema wake, ndipo abusa sadzagonekako ziweto zawo. Yeremiya 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwanira,+ ndidzabwezera mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo zolakwa zawo.+ Ndidzabwezera zolakwa za dziko la Akasidi+ ndipo dziko lawolo lidzakhala mabwinja mpaka kalekale,’+ watero Yehova. Yeremiya 51:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mizinda yake yakhala chinthu chodabwitsa, dziko lopanda madzi komanso chipululu.+ Mizindayo yakhala ngati dziko limene simukukhala munthu aliyense ndipo sipadzapezeka mwana aliyense wa munthu wodutsa mmenemo.+ Yeremiya 51:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Ndiyeno ukanene kuti, ‘Umu ndi mmene Babulo adzamirire osatulukanso chifukwa cha masoka amene ndikumugwetsera.+ Ndipo Ababulowo adzadzitopetsa okha.’”+ Mawu a Yeremiya athera pamenepa.
20 M’Babulo simudzakhalanso anthu,+ ndipo iye sadzakhalaponso ku mibadwomibadwo.+ Kumeneko Mluya sadzakhomako hema wake, ndipo abusa sadzagonekako ziweto zawo.
12 “‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwanira,+ ndidzabwezera mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo zolakwa zawo.+ Ndidzabwezera zolakwa za dziko la Akasidi+ ndipo dziko lawolo lidzakhala mabwinja mpaka kalekale,’+ watero Yehova.
43 Mizinda yake yakhala chinthu chodabwitsa, dziko lopanda madzi komanso chipululu.+ Mizindayo yakhala ngati dziko limene simukukhala munthu aliyense ndipo sipadzapezeka mwana aliyense wa munthu wodutsa mmenemo.+
64 Ndiyeno ukanene kuti, ‘Umu ndi mmene Babulo adzamirire osatulukanso chifukwa cha masoka amene ndikumugwetsera.+ Ndipo Ababulowo adzadzitopetsa okha.’”+ Mawu a Yeremiya athera pamenepa.