Yesaya 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dzikolo likulira, lafota.+ Lebanoni wachita manyazi, wanyala.+ Sharoni+ wakhala ngati chipululu ndipo Basana ndi Karimeli akuyoyola masamba awo.+ Yeremiya 50:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho nyama za m’madera opanda madzi, nyama zokonda kulira mokuwa ndi nthiwatiwa zidzakhala mmenemo.+ Simudzakhalanso munthu mmenemo ndipo mzindawo sudzapezekanso ku mibadwomibadwo.”+
9 Dzikolo likulira, lafota.+ Lebanoni wachita manyazi, wanyala.+ Sharoni+ wakhala ngati chipululu ndipo Basana ndi Karimeli akuyoyola masamba awo.+
39 Choncho nyama za m’madera opanda madzi, nyama zokonda kulira mokuwa ndi nthiwatiwa zidzakhala mmenemo.+ Simudzakhalanso munthu mmenemo ndipo mzindawo sudzapezekanso ku mibadwomibadwo.”+