Levitiko 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzabweretsa lupanga pa inu lobwezera chilango+ chifukwa cha pangano.+ Pamenepo mudzathawira m’mizinda yanu, ndipo ndidzakutumizirani mliri pakati panu+ ndi kukuperekani m’manja mwa mdani.+ Yeremiya 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Yehova sanathenso kupirira zimenezo chifukwa zochita zanu zinaipa kwambiri, chifukwa munachita zinthu zonyansa.+ Chotero dziko lanu linasanduka bwinja, chinthu chodabwitsa ndi chotembereredwa ndipo tsopano mulibe munthu wokhalamo.+ Nahumu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+
25 Ndidzabweretsa lupanga pa inu lobwezera chilango+ chifukwa cha pangano.+ Pamenepo mudzathawira m’mizinda yanu, ndipo ndidzakutumizirani mliri pakati panu+ ndi kukuperekani m’manja mwa mdani.+
22 Kenako Yehova sanathenso kupirira zimenezo chifukwa zochita zanu zinaipa kwambiri, chifukwa munachita zinthu zonyansa.+ Chotero dziko lanu linasanduka bwinja, chinthu chodabwitsa ndi chotembereredwa ndipo tsopano mulibe munthu wokhalamo.+
2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+