Salimo 89:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndani kumwamba angayerekezeredwe ndi Yehova?+Ndani angafanane ndi Yehova pakati pa ana a Mulungu?+ Yesaya 40:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi anthu inu Mulungu mungamuyerekezere ndi ndani,+ ndipo kodi mungapange chiyani choti mumufanizire nacho?+
6 Pakuti ndani kumwamba angayerekezeredwe ndi Yehova?+Ndani angafanane ndi Yehova pakati pa ana a Mulungu?+
18 Kodi anthu inu Mulungu mungamuyerekezere ndi ndani,+ ndipo kodi mungapange chiyani choti mumufanizire nacho?+