Yeremiya 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova wanena kuti: “Kodi mawu anga safanana ndi moto?+ Kodi safanana ndi nyundo imene imaphwanya thanthwe?”+ Hoseya 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chifukwa chake anthu amenewa ndidzawasema pogwiritsa ntchito aneneri.+ Ndidzawapha ndi mawu a m’kamwa mwanga.+ Chiweruzo chimene mudzalandire chidzakhala choonekera kwa anthu onse ngati kuwala.+ Chivumbulutso 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngati wina aliyense akufuna kuzivulaza, moto umatuluka m’kamwa mwawo ndi kupsereza adani awo.+ Ngati wina angafune kuzivulaza, ayenera kuphedwa mwanjira imeneyi.
29 Yehova wanena kuti: “Kodi mawu anga safanana ndi moto?+ Kodi safanana ndi nyundo imene imaphwanya thanthwe?”+
5 N’chifukwa chake anthu amenewa ndidzawasema pogwiritsa ntchito aneneri.+ Ndidzawapha ndi mawu a m’kamwa mwanga.+ Chiweruzo chimene mudzalandire chidzakhala choonekera kwa anthu onse ngati kuwala.+
5 Ngati wina aliyense akufuna kuzivulaza, moto umatuluka m’kamwa mwawo ndi kupsereza adani awo.+ Ngati wina angafune kuzivulaza, ayenera kuphedwa mwanjira imeneyi.