Luka 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mwakuti anthu adzakomoka chifukwa cha mantha+ ndi kuyembekezera zimene zichitikire dziko lapansi+ kumene kuli anthu, pakuti mphamvu zakumwamba zidzagwedezeka.+
26 Mwakuti anthu adzakomoka chifukwa cha mantha+ ndi kuyembekezera zimene zichitikire dziko lapansi+ kumene kuli anthu, pakuti mphamvu zakumwamba zidzagwedezeka.+