2 Mafumu 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 M’masiku ake, Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera kudzachita nkhondo ndi Yerusalemu. Choncho Yehoyakimu anakhala mtumiki wake+ kwa zaka zitatu, koma kenako anam’pandukira. 2 Mbiri 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehoyakimu+ anali ndi zaka 25 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wake.+
24 M’masiku ake, Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera kudzachita nkhondo ndi Yerusalemu. Choncho Yehoyakimu anakhala mtumiki wake+ kwa zaka zitatu, koma kenako anam’pandukira.
5 Yehoyakimu+ anali ndi zaka 25 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wake.+