Yesaya 30:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Anthu inu mukabwerera kwa ine n’kusiya zimene mukuchita, mudzapulumuka. Mudzakhala amphamvu mukakhala osatekeseka ndi achikhulupiriro.”+ Koma inu simunafune.+ Yeremiya 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsuka mtima wako ndi kuchotsa zoipa zonse, iwe Yerusalemu, kuti upulumuke.+ Kodi maganizo ako oipawo udzakhala nawo mpaka liti?+
15 Pakuti Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Anthu inu mukabwerera kwa ine n’kusiya zimene mukuchita, mudzapulumuka. Mudzakhala amphamvu mukakhala osatekeseka ndi achikhulupiriro.”+ Koma inu simunafune.+
14 Tsuka mtima wako ndi kuchotsa zoipa zonse, iwe Yerusalemu, kuti upulumuke.+ Kodi maganizo ako oipawo udzakhala nawo mpaka liti?+