Miyambo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Anthu osadziwa inu, kodi mukufuna kukhalabe osadziwa mpaka liti?+ Inu onyoza, mukufuna kukhalabe onyoza mpaka liti?+ Ndipo opusa inu, mudana ndi kudziwa zinthu mpaka liti?+
22 “Anthu osadziwa inu, kodi mukufuna kukhalabe osadziwa mpaka liti?+ Inu onyoza, mukufuna kukhalabe onyoza mpaka liti?+ Ndipo opusa inu, mudana ndi kudziwa zinthu mpaka liti?+