Yeremiya 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 M’mimba mwanga ine, m’mimba mwanga! Ndikumva kupweteka kwambiri mumtima mwanga.+ Mtima wanga ukuvutika.+ Sindingathe kukhala chete pakuti ndamva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, chizindikiro chochenjeza cha nkhondo.+ Yeremiya 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndasweka mtima+ chifukwa cha kuwonongeka+ kwa mwana wamkazi wa anthu anga. Ndine wachisoni. Ndadabwa kwambiri.+ Maliro 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Maso anga atopa ndi kulira.+ M’mimba mwanga mukubwadamuka.+Chiwindi changa chakhuthulidwa+ pansi chifukwa cha kuwonongedwa kwa mwana wamkazi wa anthu anga,+Ndiponso chifukwa chakuti ana ndi makanda oyamwa akukomoka+ m’mabwalo a mzinda.
19 M’mimba mwanga ine, m’mimba mwanga! Ndikumva kupweteka kwambiri mumtima mwanga.+ Mtima wanga ukuvutika.+ Sindingathe kukhala chete pakuti ndamva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, chizindikiro chochenjeza cha nkhondo.+
21 Ndasweka mtima+ chifukwa cha kuwonongeka+ kwa mwana wamkazi wa anthu anga. Ndine wachisoni. Ndadabwa kwambiri.+
11 Maso anga atopa ndi kulira.+ M’mimba mwanga mukubwadamuka.+Chiwindi changa chakhuthulidwa+ pansi chifukwa cha kuwonongedwa kwa mwana wamkazi wa anthu anga,+Ndiponso chifukwa chakuti ana ndi makanda oyamwa akukomoka+ m’mabwalo a mzinda.