Yobu 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mkwiyo wa Mulungu wandikhadzula. Iye ali nane chidani+Ndipo akundikukutira mano.+Mdani wanga akundiyang’ana ndi diso lozonda.+ Salimo 37:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Woipa akukonzera chiwembu munthu wolungama,+Ndipo akumukukutira mano.+ Machitidwe 7:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Atamva zimenezi, anakwiya koopsa+ ndipo anayamba kumukukutira+ mano.
9 Mkwiyo wa Mulungu wandikhadzula. Iye ali nane chidani+Ndipo akundikukutira mano.+Mdani wanga akundiyang’ana ndi diso lozonda.+