Yobu 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo ayasamula kukamwa kwawo kuti andimeze.+Andimenya mbama ndi mnyozo.Asonkhana ambirimbiri kuti alimbane nane.+ Salimo 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo anditsegulira pakamwa pawo mondiopseza,+Ngati mkango wokhadzula nyama umenenso ukubangula.+ Maliro 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adani ako onse akukutsegulira pakamwa.+Akuimba mluzu ndi kukukukutira mano.+ Iwo akunena kuti: “Ameneyu timumeza.+Ndithu, lero ndi tsiku limene takhala tikuyembekezera.+ Lafikadi! Taliona!”+
10 Iwo ayasamula kukamwa kwawo kuti andimeze.+Andimenya mbama ndi mnyozo.Asonkhana ambirimbiri kuti alimbane nane.+
16 Adani ako onse akukutsegulira pakamwa.+Akuimba mluzu ndi kukukukutira mano.+ Iwo akunena kuti: “Ameneyu timumeza.+Ndithu, lero ndi tsiku limene takhala tikuyembekezera.+ Lafikadi! Taliona!”+