Salimo 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zingwe za imfa zinandikulunga,+Chikhamu cha anthu opanda pake chinali kundiopseza.+ Salimo 69:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndamila m’matope akuya, mmene mulibe malo oponda.+Ndalowa m’madzi akuya,Ndipo mtsinje wa madzi othamanga wandikokolola.+ Salimo 88:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zandizungulira ngati madzi tsiku lonse.+Zandimiza pa nthawi imodzi. Salimo 124:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo madzi akanatikokolola,+Mtsinje wamphamvu ukanatimiza.+
2 Ndamila m’matope akuya, mmene mulibe malo oponda.+Ndalowa m’madzi akuya,Ndipo mtsinje wa madzi othamanga wandikokolola.+