Levitiko 26:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iwo adzagwetsana okhaokha ngati kuti akuthawa lupanga, koma popanda munthu wowathamangitsa. Simudzatha n’komwe kulimbana ndi adani anu.+ Yeremiya 52:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ziwerengero za anthu amene Nebukadirezara anawatenga kupita nawo ku ukapolo ndi izi: m’chaka cha 7 cha ulamuliro wake, anatenga Ayuda 3,023.+ Ezekieli 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ndithu ine ndidzakutulutsani mumzindawu n’kukuperekani m’manja mwa alendo,+ ndipo ndidzakulangani.+
37 Iwo adzagwetsana okhaokha ngati kuti akuthawa lupanga, koma popanda munthu wowathamangitsa. Simudzatha n’komwe kulimbana ndi adani anu.+
28 Ziwerengero za anthu amene Nebukadirezara anawatenga kupita nawo ku ukapolo ndi izi: m’chaka cha 7 cha ulamuliro wake, anatenga Ayuda 3,023.+
9 ‘Ndithu ine ndidzakutulutsani mumzindawu n’kukuperekani m’manja mwa alendo,+ ndipo ndidzakulangani.+