Ezekieli 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Tsoka mzinda wokhetsa magazi,+ umene uli ngati mphika wakukamwa kwakukulu. Mphikawo uli ndi dzimbiri ndipo dzimbiri lakelo silikutha. Muchotsemo nthulizo imodziimodzi.+ Musachite maere pamphikawo.+
6 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Tsoka mzinda wokhetsa magazi,+ umene uli ngati mphika wakukamwa kwakukulu. Mphikawo uli ndi dzimbiri ndipo dzimbiri lakelo silikutha. Muchotsemo nthulizo imodziimodzi.+ Musachite maere pamphikawo.+