Ezekieli 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Anthu ophedwa amene mwawaika pakati pa mzindawu ndiwo nyama.+ Mzindawu ndiwo mphika wakukamwa kwakukulu.+ Koma inuyo mudzatulutsidwa mumzindawu.’”+ Ezekieli 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ndithu ine ndidzakutulutsani mumzindawu n’kukuperekani m’manja mwa alendo,+ ndipo ndidzakulangani.+
7 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Anthu ophedwa amene mwawaika pakati pa mzindawu ndiwo nyama.+ Mzindawu ndiwo mphika wakukamwa kwakukulu.+ Koma inuyo mudzatulutsidwa mumzindawu.’”+
9 ‘Ndithu ine ndidzakutulutsani mumzindawu n’kukuperekani m’manja mwa alendo,+ ndipo ndidzakulangani.+