Ezekieli 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anapitiriza kuchita zauhule zakezo ndi amuna onse osankhidwa a ku Asuri. Anadziipitsa ndi amuna onse amene anawakhumba ndiponso ndi mafano awo onyansa.+
7 Iye anapitiriza kuchita zauhule zakezo ndi amuna onse osankhidwa a ku Asuri. Anadziipitsa ndi amuna onse amene anawakhumba ndiponso ndi mafano awo onyansa.+