Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndithu ndidzayeza Yerusalemu ndi chingwe chimene ndinayezera+ Samariya,+ ndiponso ndidzamuyeza ndi thabwa lowongolera limene ndinayezera nyumba ya Ahabu.+ Yerusalemu ndidzam’pukuta+ mpaka kuyera mbee ngati mmene munthu amapukutira mbale yolowa mpaka kuyera mbee, n’kuitembenuza.+

  • Salimo 11:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Iye adzavumbitsira oipa misampha, moto ndi sulufule,+

      Komanso mphepo yotentha, monga gawo limene ayenera kumwa.+

  • Yeremiya 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ine ndidzakuthamangitsani, kukuchotsani pamaso panga,+ ngati mmene ndinathamangitsira abale anu onse, mbadwa zonse za Efuraimu.’+

  • Yeremiya 25:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova Mulungu wa Isiraeli anandiuza kuti: “Landira chikho ichi chimene chili m’dzanja langa. Mmenemu muli vinyo wa mkwiyo ndipo ukamwetse mitundu yonse imene ndikukutumizako.+

  • Danieli 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Inu munachitadi zimene munachenjeza kuti mudzatichitira,+ ifeyo ndi atsogoleri athu.+ Munatigwetsera tsoka lalikulu ndipo tsoka limene lagwera Yerusalemu silinachitikeponso padziko lonse lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena