Levitiko 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Otsala pakati panu, adzazunzika+ chifukwa cha zolakwa zawo m’mayiko a adani awo. Iwo adzazunzika chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ mmene makolowo anazunzikira. Ezekieli 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 mwakuti chakudya ndi madzi zidzakhala zosowa. Azidzayang’anizana modabwa ndipo adzaonda chifukwa cha zolakwa zawo.+ Ezekieli 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Choncho iwe mwana wa munthu, uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Anthu inu mwanena kuti: “Tingakhale bwanji ndi moyo, popeza kuti kupanduka kwathu ndi machimo athu zili pa ife ndipo tikuwola+ chifukwa cha zimenezi?”’+
39 Otsala pakati panu, adzazunzika+ chifukwa cha zolakwa zawo m’mayiko a adani awo. Iwo adzazunzika chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ mmene makolowo anazunzikira.
17 mwakuti chakudya ndi madzi zidzakhala zosowa. Azidzayang’anizana modabwa ndipo adzaonda chifukwa cha zolakwa zawo.+
10 “Choncho iwe mwana wa munthu, uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Anthu inu mwanena kuti: “Tingakhale bwanji ndi moyo, popeza kuti kupanduka kwathu ndi machimo athu zili pa ife ndipo tikuwola+ chifukwa cha zimenezi?”’+