Levitiko 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Otsala pakati panu, adzazunzika+ chifukwa cha zolakwa zawo m’mayiko a adani awo. Iwo adzazunzika chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ mmene makolowo anazunzikira. Ezekieli 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mudzavala chovala chakumutu ndiponso nsapato zanu. Simudzadziguguda pachifuwa kapena kulira.+ Mudzawonda chifukwa cha zolakwa zanu+ ndipo mudzabuula pakati panu.+
39 Otsala pakati panu, adzazunzika+ chifukwa cha zolakwa zawo m’mayiko a adani awo. Iwo adzazunzika chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ mmene makolowo anazunzikira.
23 Mudzavala chovala chakumutu ndiponso nsapato zanu. Simudzadziguguda pachifuwa kapena kulira.+ Mudzawonda chifukwa cha zolakwa zanu+ ndipo mudzabuula pakati panu.+