Levitiko 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Otsala pakati panu, adzazunzika+ chifukwa cha zolakwa zawo m’mayiko a adani awo. Iwo adzazunzika chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ mmene makolowo anazunzikira. Yesaya 64:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tonsefe takhala ngati munthu wodetsedwa, ndipo zochita zathu zonse zolungama zili ngati kansalu kamene mkazi amavala pa nthawi yosamba.+ Tonsefe tidzayoyoka ngati masamba+ ndipo zolakwa zathu zidzatiuluzira kutali ngati mphepo.+ Ezekieli 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mudzavala chovala chakumutu ndiponso nsapato zanu. Simudzadziguguda pachifuwa kapena kulira.+ Mudzawonda chifukwa cha zolakwa zanu+ ndipo mudzabuula pakati panu.+
39 Otsala pakati panu, adzazunzika+ chifukwa cha zolakwa zawo m’mayiko a adani awo. Iwo adzazunzika chifukwa cha zolakwa za makolo awo,+ mmene makolowo anazunzikira.
6 Tonsefe takhala ngati munthu wodetsedwa, ndipo zochita zathu zonse zolungama zili ngati kansalu kamene mkazi amavala pa nthawi yosamba.+ Tonsefe tidzayoyoka ngati masamba+ ndipo zolakwa zathu zidzatiuluzira kutali ngati mphepo.+
23 Mudzavala chovala chakumutu ndiponso nsapato zanu. Simudzadziguguda pachifuwa kapena kulira.+ Mudzawonda chifukwa cha zolakwa zanu+ ndipo mudzabuula pakati panu.+