Ezekieli 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako chinatenga zina mwa mbewu za m’dzikomo+ ndi kuzibzala m’munda wolimidwa bwino. Chinabzala nsonga ya mkungudza ija ngati mtengo wa msondodzi umene uli m’mphepete mwa madzi ambiri.+
5 Kenako chinatenga zina mwa mbewu za m’dzikomo+ ndi kuzibzala m’munda wolimidwa bwino. Chinabzala nsonga ya mkungudza ija ngati mtengo wa msondodzi umene uli m’mphepete mwa madzi ambiri.+