Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo mfumu ya Isiraeli inatumiza anthu kumalo amene munthu wa Mulungu woona uja anaiuza.+ Elisa anachenjeza+ mfumu ya Isiraeli ndipo sinapiteko. Izi zinachitika kangapo, osati kamodzi kapena kawiri kokha.

  • Aheberi 11:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mwa chikhulupiriro, Nowa+ atachenjezedwa ndi Mulungu za zinthu zimene zinali zisanaoneke,+ anasonyeza kuopa Mulungu ndipo anamanga chingalawa+ kuti banja lake lipulumukiremo. Mwa chikhulupiriro chimenecho, anatsutsa dziko,+ ndipo anakhala wolandira cholowa cha chilungamo,+ chimene chimabwera ndi chikhulupiriro.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena