Yeremiya 44:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Popeza munachimwira Yehova,+ munali kupereka nsembe zautsi+ ndipo simunamvere mawu a Yehova+ ndi kutsatira malamulo ake,+ malangizo ake ndi zikumbutso zake, n’chifukwa chake masoka onsewa akugwerani lero.”+
23 Popeza munachimwira Yehova,+ munali kupereka nsembe zautsi+ ndipo simunamvere mawu a Yehova+ ndi kutsatira malamulo ake,+ malangizo ake ndi zikumbutso zake, n’chifukwa chake masoka onsewa akugwerani lero.”+