Salimo 80:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+ Yesaya 56:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mawu a Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, amene akusonkhanitsa pamodzi Aisiraeli omwe anabalalitsidwa,+ ndi akuti: “Ine ndidzamusonkhanitsiranso anthu ena kuwonjezera pa anthu ake amene anasonkhanitsidwa kale.”+
80 Inu M’busa wa Isiraeli, tcherani khutu,+Inu amene mukutsogolera Yosefe ngati gulu la nkhosa.+Inu amene mwakhala pa akerubi,+ walani.+
8 Mawu a Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, amene akusonkhanitsa pamodzi Aisiraeli omwe anabalalitsidwa,+ ndi akuti: “Ine ndidzamusonkhanitsiranso anthu ena kuwonjezera pa anthu ake amene anasonkhanitsidwa kale.”+