Salimo 74:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, kodi mdani adzakuchitirani mopanda ulemu kufikira liti?+Kodi mdani adzanyoza dzina lanu kwamuyaya?+ Salimo 123:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moyo wathu wasautsika kwambiri chifukwa cha kunyoza kwa anthu amene akukhala mosatekeseka,+Ndiponso chifukwa cha kunyoza kwa anthu odzikuza.+ Ezekieli 34:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘“Ndidzawapatsa munda wotchuka+ ndipo sadzafa ndi njala m’dzikomo.+ Mitundu ina ya anthu sidzawanyozanso.+
10 Inu Mulungu, kodi mdani adzakuchitirani mopanda ulemu kufikira liti?+Kodi mdani adzanyoza dzina lanu kwamuyaya?+
4 Moyo wathu wasautsika kwambiri chifukwa cha kunyoza kwa anthu amene akukhala mosatekeseka,+Ndiponso chifukwa cha kunyoza kwa anthu odzikuza.+
29 “‘“Ndidzawapatsa munda wotchuka+ ndipo sadzafa ndi njala m’dzikomo.+ Mitundu ina ya anthu sidzawanyozanso.+