Yesaya 65:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Sadzagwira ntchito pachabe+ komanso sadzaberekera tsoka,+ chifukwa iwo ndiponso ana awo+ ndi odalitsidwa ndi Yehova.+ Yeremiya 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipeta anthu anga ngati mbewu kuzipata za m’dzikoli. Ndithu, ndiwauluza ndi chifoloko.+ Ndiwaphera ana awo+ ndipo ndiwononga anthu anga chifukwa sanasiye kuchita zinthu zoipa.+
23 Sadzagwira ntchito pachabe+ komanso sadzaberekera tsoka,+ chifukwa iwo ndiponso ana awo+ ndi odalitsidwa ndi Yehova.+
7 Ndipeta anthu anga ngati mbewu kuzipata za m’dzikoli. Ndithu, ndiwauluza ndi chifoloko.+ Ndiwaphera ana awo+ ndipo ndiwononga anthu anga chifukwa sanasiye kuchita zinthu zoipa.+