Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 89:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Inu Yehova, kumbukirani chitonzo chimene chagwera atumiki anu.+

      Kumbukirani kuti ndanyamula pachifuwa panga chitonzo cha mitundu yambiri ya anthu.+

  • Ezekieli 36:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Pamenepo iwo anapita kwa anthu a mitundu ina ndipo anthuwo anayamba kudetsa dzina langa loyera+ ponena za iwowo kuti, ‘Awa ndi anthu a Yehova, ndipo anachoka m’dziko lake.’+

  • Ezekieli 36:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndidzamva chisoni chifukwa cha dzina langa loyera limene nyumba ya Isiraeli yalidetsa pakati pa anthu a mitundu ina kumene iwo anapita.”+

  • Zefaniya 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Ndamva chitonzo cha Mowabu+ ndi mawu onyoza a ana a Amoni+ amene anali kunena kwa anthu anga. Iwo anali kuopseza anthu anga modzitukumula kuti awalanda dziko lawo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena