Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Onani tsopano kuti ndine Mulungu,+

      Ndipo palibe milungu ina pamodzi ndi ine.+

      Ndimapha ndiponso ndimapereka moyo.+

      Ndavulaza koopsa,+ ndipo ine ndidzachiritsa,+

      Palibe aliyense wonditsomphola m’dzanja langa.+

  • 1 Samueli 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Yehova ndi Wakupha ndi Wosunga moyo,+

      Iye ndi Wotsitsira Kumanda,+ ndiponso Woukitsa.+

  • Aroma 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 monga mmene Malemba amanenera kuti: “Ndakuika kuti ukhale tate wa mitundu yambiri.”)+ Izi zinali choncho pamaso pa Uyo amene Abulahamu anam’khulupirira, inde pamaso pa Mulungu, amene amapereka moyo kwa akufa+ ndipo amanena za zinthu zimene palibe ngati kuti zilipo.+

  • 2 Akorinto 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ngakhalenso m’mitima mwathu, tinali kumva ngati talandira chiweruzo cha imfa. Zinatero kuti tisakhale ndi chikhulupiriro mwa ife tokha,+ koma mwa Mulungu amene amaukitsa akufa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena