Salimo 126:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyo tinaseka kwambiri,+Ndipo lilime lathu linatulutsa mawu okondwa.+Pamenepo anthu a mitundu ina anayamba kuuzana kuti:+“Yehova wachitira anthu amenewa zinthu zazikulu.”+ Ezekieli 37:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzakuikirani mitsempha ndi kukupatsani mnofu. Ndidzakukutani ndi khungu ndi kuika mpweya mwa inu ndipo mudzakhala ndi moyo.+ Choncho mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+
2 Pa nthawiyo tinaseka kwambiri,+Ndipo lilime lathu linatulutsa mawu okondwa.+Pamenepo anthu a mitundu ina anayamba kuuzana kuti:+“Yehova wachitira anthu amenewa zinthu zazikulu.”+
6 Ndidzakuikirani mitsempha ndi kukupatsani mnofu. Ndidzakukutani ndi khungu ndi kuika mpweya mwa inu ndipo mudzakhala ndi moyo.+ Choncho mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+