Ezekieli 39:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu ongodutsa akamadzadutsa m’dzikolo, wina n’kuona fupa la munthu, azidzaikapo chizindikiro mpaka anthu ofotsera aja atakafotsera fupalo m’Chigwa cha Khamu la Gogi.+
15 Anthu ongodutsa akamadzadutsa m’dzikolo, wina n’kuona fupa la munthu, azidzaikapo chizindikiro mpaka anthu ofotsera aja atakafotsera fupalo m’Chigwa cha Khamu la Gogi.+