-
Ezekieli 39:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 “‘Pa tsiku limenelo Gogi+ ndidzam’patsa malo kuti akhale manda ake mu Isiraeli. Ndidzam’patsa chigwa cha kum’mawa kwa nyanja, chomwe ndi chigwa cha anthu ongodutsa. Chigwacho chidzatseka njira ya anthu ongodutsawo. Kumeneko iwo adzaika m’manda Gogi pamodzi ndi khamu lake lonse, ndipo adzatcha chigwacho kuti Chigwa cha Khamu la Gogi.+
-